Yesaya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anakhudza pakamwa panga+ n’kunena kuti: “Taona! Khalali lakhudza milomo yako, chotero zolakwa zako zachoka ndipo machimo ako aphimbidwa.”+ Yeremiya 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Yehova anatambasula dzanja lake ndi kukhudza pakamwa panga.+ Ndiyeno Yehova anandiuza kuti: “Ndaika mawu anga m’kamwa mwako.+
7 Iye anakhudza pakamwa panga+ n’kunena kuti: “Taona! Khalali lakhudza milomo yako, chotero zolakwa zako zachoka ndipo machimo ako aphimbidwa.”+
9 Pamenepo Yehova anatambasula dzanja lake ndi kukhudza pakamwa panga.+ Ndiyeno Yehova anandiuza kuti: “Ndaika mawu anga m’kamwa mwako.+