Salimo 51:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mundisambitse bwinobwino ndi kuchotsa cholakwa changa,+Ndiyeretseni ku tchimo langa.+ Mika 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu+ amene amakhululukira zolakwa+ ndi machimo a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale, pakuti kusonyeza kukoma mtima kosatha kumakusangalatsani.+ Zekariya 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno mngeloyo anauza amene anaimirira pamaso pake kuti: “Muvuleni zovala zonyansazi.” Kenako anauza Yoswa kuti: “Waona, ndakuchotsera zolakwa zako,+ ndipo wavekedwa mikanjo yapadera.”+
18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu+ amene amakhululukira zolakwa+ ndi machimo a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale, pakuti kusonyeza kukoma mtima kosatha kumakusangalatsani.+
4 Ndiyeno mngeloyo anauza amene anaimirira pamaso pake kuti: “Muvuleni zovala zonyansazi.” Kenako anauza Yoswa kuti: “Waona, ndakuchotsera zolakwa zako,+ ndipo wavekedwa mikanjo yapadera.”+