Ezekieli 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anthu onse omuzungulira amene amamuthandiza, ndiponso magulu ake onse ankhondo, ndidzawabalalitsira ku mphepo zonse zinayi,+ ndipo ndidzawatsatira nditasolola lupanga.+ Ezekieli 17:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Gulu lonse la asilikali ake amene anathawa, lidzaphedwa ndi lupanga. Amene adzapulumuke adzabalalikira ku mphepo zonse.+ Anthu inu mudzadziwa kuti ine Yehova ndi amene ndanena zimenezi.”’+
14 Anthu onse omuzungulira amene amamuthandiza, ndiponso magulu ake onse ankhondo, ndidzawabalalitsira ku mphepo zonse zinayi,+ ndipo ndidzawatsatira nditasolola lupanga.+
21 Gulu lonse la asilikali ake amene anathawa, lidzaphedwa ndi lupanga. Amene adzapulumuke adzabalalikira ku mphepo zonse.+ Anthu inu mudzadziwa kuti ine Yehova ndi amene ndanena zimenezi.”’+