Danieli 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo mfumu inayamba kulankhula nawo ndipo pa ana onsewo, palibe aliyense amene anali ngati Danieli, Hananiya, Misayeli ndi Azariya.+ Chotero ana amenewa anapitiriza kutumikira mfumu.+ Danieli 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chotero Danieli anapita kwa mfumu kukapempha kuti imupatse nthawi kuti adzamasulire maloto ake.+
19 Pamenepo mfumu inayamba kulankhula nawo ndipo pa ana onsewo, palibe aliyense amene anali ngati Danieli, Hananiya, Misayeli ndi Azariya.+ Chotero ana amenewa anapitiriza kutumikira mfumu.+