Danieli 2:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “Pambuyo panu padzabwera ufumu wina+ wotsikirapo kwa inu.+ Kenako padzabweranso ufumu wina wachitatu, wamkuwa, umene udzalamulira dziko lonse lapansi.+ Danieli 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “PERESI,* ufumu wanu wagawanika ndipo waperekedwa kwa Amedi ndi Aperisiya.”+ Danieli 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Ndinaonanso chilombo china chachiwiri, chooneka ngati chimbalangondo.+ Chinali chotukuka mbali imodzi+ ndipo m’kamwa mwake munali nthiti zitatu pakati pa mano ake. Chilombochi chinauzidwa kuti, ‘Nyamuka, idya nyama yambiri.’+ Danieli 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nditakweza maso anga ndinaona nkhosa yamphongo+ itaimirira pafupi ndi mtsinjewo ndipo inali ndi nyanga ziwiri. Nyanga ziwirizi zinali zazitali koma imodzi, imene inamera pomalizira, inali yaitali kuposa inzake.+
39 “Pambuyo panu padzabwera ufumu wina+ wotsikirapo kwa inu.+ Kenako padzabweranso ufumu wina wachitatu, wamkuwa, umene udzalamulira dziko lonse lapansi.+
5 “Ndinaonanso chilombo china chachiwiri, chooneka ngati chimbalangondo.+ Chinali chotukuka mbali imodzi+ ndipo m’kamwa mwake munali nthiti zitatu pakati pa mano ake. Chilombochi chinauzidwa kuti, ‘Nyamuka, idya nyama yambiri.’+
3 Nditakweza maso anga ndinaona nkhosa yamphongo+ itaimirira pafupi ndi mtsinjewo ndipo inali ndi nyanga ziwiri. Nyanga ziwirizi zinali zazitali koma imodzi, imene inamera pomalizira, inali yaitali kuposa inzake.+