Ezekieli 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Unali kutenga zinthu zako zokongola zochokera pagolide ndi siliva wanga amene ndinakupatsa+ n’kupangira zifaniziro za munthu wamwamuna+ n’kumachita nazo uhule.+
17 Unali kutenga zinthu zako zokongola zochokera pagolide ndi siliva wanga amene ndinakupatsa+ n’kupangira zifaniziro za munthu wamwamuna+ n’kumachita nazo uhule.+