Mika 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu okhulupirika atha padziko lapansi, ndipo pakati pa anthu palibe munthu wowongoka mtima.+ Onse amadikirira anzawo kuti akhetse magazi.+ Aliyense amasaka m’bale wake ndi ukonde.+ Habakuku 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mdani amagwira zonsezi ndi mbedza+ ndipo amazikokolola ndi khoka lake n’kuzisonkhanitsa muukonde wake wophera nsomba.+ N’chifukwa chake iye amasangalala ndipo amakhala wokondwa.+
2 Anthu okhulupirika atha padziko lapansi, ndipo pakati pa anthu palibe munthu wowongoka mtima.+ Onse amadikirira anzawo kuti akhetse magazi.+ Aliyense amasaka m’bale wake ndi ukonde.+
15 Mdani amagwira zonsezi ndi mbedza+ ndipo amazikokolola ndi khoka lake n’kuzisonkhanitsa muukonde wake wophera nsomba.+ N’chifukwa chake iye amasangalala ndipo amakhala wokondwa.+