2 Mafumu 19:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndithu ndidzateteza+ mzinda uno kuti ndiupulumutse chifukwa cha ine mwini+ ndiponso chifukwa cha Davide mtumiki wanga.”’”+ Hoseya 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Efuraimu amalankhula mabodza okhaokha kwa ine.+ Kulikonse kumene ndingayang’ane ndikuona chinyengo cha Isiraeli, koma Yuda akuyendabe ndi Mulungu+ ndipo iye ndi wokhulupirika kwa Woyera Koposa.”
34 Ndithu ndidzateteza+ mzinda uno kuti ndiupulumutse chifukwa cha ine mwini+ ndiponso chifukwa cha Davide mtumiki wanga.”’”+
12 “Efuraimu amalankhula mabodza okhaokha kwa ine.+ Kulikonse kumene ndingayang’ane ndikuona chinyengo cha Isiraeli, koma Yuda akuyendabe ndi Mulungu+ ndipo iye ndi wokhulupirika kwa Woyera Koposa.”