Salimo 31:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma ine chikhulupiriro changa chili mwa inu Yehova.+Ndipo ndikunena kuti: “Inu ndinu Mulungu wanga.”+ Yesaya 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chotero mneneriyo anati: “Tamverani inu a nyumba ya Davide. Kodi mukuona ngati n’zazing’ono kuti muzitopetsa anthu, ndiponso kuti mutopetse Mulungu wanga?+ Mika 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma ine ndidzadikirira Yehova.+ Ndidzayembekezera moleza mtima Mulungu wa chipulumutso changa.+ Mulungu wanga adzandimvera.+
14 Koma ine chikhulupiriro changa chili mwa inu Yehova.+Ndipo ndikunena kuti: “Inu ndinu Mulungu wanga.”+
13 Chotero mneneriyo anati: “Tamverani inu a nyumba ya Davide. Kodi mukuona ngati n’zazing’ono kuti muzitopetsa anthu, ndiponso kuti mutopetse Mulungu wanga?+
7 Koma ine ndidzadikirira Yehova.+ Ndidzayembekezera moleza mtima Mulungu wa chipulumutso changa.+ Mulungu wanga adzandimvera.+