Yesaya 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikufuna ndimuimbire nyimbo munthu amene ndimamukonda. Imeneyi ndi nyimbo yonena za munthu amene ndimamukonda, ndiponso munda wake wa mpesa.+ Wokondedwa wanga anali ndi munda wa mpesa pamalo achonde m’mbali mwa phiri. Ezekieli 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Mofanana ndi mtengo wa mpesa umene uli pakati pa nkhalango, umene ndaupereka kuti uzikhala nkhuni pamoto, ndaperekanso anthu okhala mu Yerusalemu.+
5 Ndikufuna ndimuimbire nyimbo munthu amene ndimamukonda. Imeneyi ndi nyimbo yonena za munthu amene ndimamukonda, ndiponso munda wake wa mpesa.+ Wokondedwa wanga anali ndi munda wa mpesa pamalo achonde m’mbali mwa phiri.
6 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Mofanana ndi mtengo wa mpesa umene uli pakati pa nkhalango, umene ndaupereka kuti uzikhala nkhuni pamoto, ndaperekanso anthu okhala mu Yerusalemu.+