Yesaya 55:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu inu funafunani Yehova pamene iye akupezekabe.+ Muitaneni akadali pafupi.+ Amosi 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Yehova wauza anthu a m’nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Yesetsani kundiyandikira,+ kuti mupitirize kukhala ndi moyo.+
4 “Yehova wauza anthu a m’nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Yesetsani kundiyandikira,+ kuti mupitirize kukhala ndi moyo.+