Miyambo 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wofesa zosalungama adzakolola zopweteka,+ ndipo ndodo ya ukali wake idzatha.+ Hoseya 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Iwo akungofesa mphepo, ndipo adzakolola mphepo yamkuntho.+ Tirigu amene ali m’minda yawo sakukula.+ Mbewu zawo sizikuwapatsa ufa.+ Ngati zina mwa mbewuzo zingabereke, alendo adzazimeza.+
7 “Iwo akungofesa mphepo, ndipo adzakolola mphepo yamkuntho.+ Tirigu amene ali m’minda yawo sakukula.+ Mbewu zawo sizikuwapatsa ufa.+ Ngati zina mwa mbewuzo zingabereke, alendo adzazimeza.+