Yeremiya 31:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Ndamva Efuraimu akudzilirira+ kuti, ‘Mwandidzudzula kuti ndiwongolere.+ Ndinali ngati mwana wa ng’ombe wosaphunzitsidwa.+ Ndithandizeni kubwerera ndipo ndidzabwereradi,+ pakuti inu ndinu Yehova Mulungu wanga.+ Hoseya 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako ndidzabwerera kumalo anga kufikira iwo atalangidwa chifukwa cha zolakwa zawo+ ndipo adzayamba kufunafuna nkhope yanga.+ Zinthu zikadzawavuta,+ adzandifuna.”+ Luka 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Basi ndinyamuka ndizipita+ kwa bambo anga ndikawauze kuti: “Bambo, ndachimwira kumwamba komanso ndachimwira inu.+
18 “Ndamva Efuraimu akudzilirira+ kuti, ‘Mwandidzudzula kuti ndiwongolere.+ Ndinali ngati mwana wa ng’ombe wosaphunzitsidwa.+ Ndithandizeni kubwerera ndipo ndidzabwereradi,+ pakuti inu ndinu Yehova Mulungu wanga.+
15 Kenako ndidzabwerera kumalo anga kufikira iwo atalangidwa chifukwa cha zolakwa zawo+ ndipo adzayamba kufunafuna nkhope yanga.+ Zinthu zikadzawavuta,+ adzandifuna.”+
18 Basi ndinyamuka ndizipita+ kwa bambo anga ndikawauze kuti: “Bambo, ndachimwira kumwamba komanso ndachimwira inu.+