Yeremiya 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ‘Ndithudi, monga mmene mkazi amasiyira mwamuna wake+ mwachinyengo, inunso a m’nyumba ya Isiraeli mwandichitira zachinyengo,’+ watero Yehova.” Hoseya 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo Hoseya anapita ndi kukakwatira Gomeri, mwana wamkazi wa Dibulaimu. Kenako Gomeri anatenga pakati ndipo anamuberekera mwana wamwamuna.+
20 ‘Ndithudi, monga mmene mkazi amasiyira mwamuna wake+ mwachinyengo, inunso a m’nyumba ya Isiraeli mwandichitira zachinyengo,’+ watero Yehova.”
3 Pamenepo Hoseya anapita ndi kukakwatira Gomeri, mwana wamkazi wa Dibulaimu. Kenako Gomeri anatenga pakati ndipo anamuberekera mwana wamwamuna.+