Yesaya 48:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Komanso, inu simunafune kumva+ kapena kumvetsa zimenezi. Kuyambira pa nthawi imeneyo kupita m’tsogolo, simunatsegule khutu lanu. Pakuti ine ndinkadziwa ndithu kuti inu munali kuchita zachinyengo,+ ndipo mwatchedwa ‘wochimwa chibadwire.’+ Yeremiya 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti a m’nyumba ya Isiraeli ndi a m’nyumba ya Yuda andichitiradi zachinyengo,” watero Yehova.+ Hoseya 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Achitira Yehova zinthu zachinyengo,+ chifukwa abereka ana achilendo.+ Tsopano pomatha mwezi, iwo adzakhala atadyedwa limodzi ndi zinthu zawo.+ Hoseya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma iwo, mofanana ndi munthu wochokera kufumbi, aphwanya pangano.+ Andichitira zachinyengo kumalo kumene amakhala.+ Malaki 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yuda wachita zachinyengo, ndipo mu Isiraeli ndi mu Yerusalemu mwachitika zinthu zonyansa.+ Pakuti Yuda wadetsa chiyero cha Yehova+ chimene Mulungu amachikonda, ndipo Yuda wakwatira mwana wamkazi wa mulungu wachilendo.+
8 “Komanso, inu simunafune kumva+ kapena kumvetsa zimenezi. Kuyambira pa nthawi imeneyo kupita m’tsogolo, simunatsegule khutu lanu. Pakuti ine ndinkadziwa ndithu kuti inu munali kuchita zachinyengo,+ ndipo mwatchedwa ‘wochimwa chibadwire.’+
7 Achitira Yehova zinthu zachinyengo,+ chifukwa abereka ana achilendo.+ Tsopano pomatha mwezi, iwo adzakhala atadyedwa limodzi ndi zinthu zawo.+
7 Koma iwo, mofanana ndi munthu wochokera kufumbi, aphwanya pangano.+ Andichitira zachinyengo kumalo kumene amakhala.+
11 Yuda wachita zachinyengo, ndipo mu Isiraeli ndi mu Yerusalemu mwachitika zinthu zonyansa.+ Pakuti Yuda wadetsa chiyero cha Yehova+ chimene Mulungu amachikonda, ndipo Yuda wakwatira mwana wamkazi wa mulungu wachilendo.+