Yesaya 48:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Komanso, inu simunafune kumva+ kapena kumvetsa zimenezi. Kuyambira pa nthawi imeneyo kupita m’tsogolo, simunatsegule khutu lanu. Pakuti ine ndinkadziwa ndithu kuti inu munali kuchita zachinyengo,+ ndipo mwatchedwa ‘wochimwa chibadwire.’+ Yeremiya 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ‘Ndithudi, monga mmene mkazi amasiyira mwamuna wake+ mwachinyengo, inunso a m’nyumba ya Isiraeli mwandichitira zachinyengo,’+ watero Yehova.” Hoseya 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Achitira Yehova zinthu zachinyengo,+ chifukwa abereka ana achilendo.+ Tsopano pomatha mwezi, iwo adzakhala atadyedwa limodzi ndi zinthu zawo.+ Hoseya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma iwo, mofanana ndi munthu wochokera kufumbi, aphwanya pangano.+ Andichitira zachinyengo kumalo kumene amakhala.+
8 “Komanso, inu simunafune kumva+ kapena kumvetsa zimenezi. Kuyambira pa nthawi imeneyo kupita m’tsogolo, simunatsegule khutu lanu. Pakuti ine ndinkadziwa ndithu kuti inu munali kuchita zachinyengo,+ ndipo mwatchedwa ‘wochimwa chibadwire.’+
20 ‘Ndithudi, monga mmene mkazi amasiyira mwamuna wake+ mwachinyengo, inunso a m’nyumba ya Isiraeli mwandichitira zachinyengo,’+ watero Yehova.”
7 Achitira Yehova zinthu zachinyengo,+ chifukwa abereka ana achilendo.+ Tsopano pomatha mwezi, iwo adzakhala atadyedwa limodzi ndi zinthu zawo.+
7 Koma iwo, mofanana ndi munthu wochokera kufumbi, aphwanya pangano.+ Andichitira zachinyengo kumalo kumene amakhala.+