Deuteronomo 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndipo Yehova adzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo mudzatsala ochepa+ m’mayiko a mitundu imene Yehova adzakuingitsiraniko. Deuteronomo 28:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Ngakhale kuti mwachuluka ngati nyenyezi zakumwamba,+ mudzatsala ochepa+ chifukwa chosamvera mawu a Yehova Mulungu wanu. Yesaya 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti iwe Isiraeli, ngakhale anthu ako atakhala ngati mchenga wa kunyanja,+ otsala ochepa okha pakati pawo ndi amene adzabwerere.+ Chiwonongeko+ chimene Mulungu wakonzera anthu awa chidzabwera mwachilungamo ngati madzi osefukira,+
27 Ndipo Yehova adzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo mudzatsala ochepa+ m’mayiko a mitundu imene Yehova adzakuingitsiraniko.
62 Ngakhale kuti mwachuluka ngati nyenyezi zakumwamba,+ mudzatsala ochepa+ chifukwa chosamvera mawu a Yehova Mulungu wanu.
22 Pakuti iwe Isiraeli, ngakhale anthu ako atakhala ngati mchenga wa kunyanja,+ otsala ochepa okha pakati pawo ndi amene adzabwerere.+ Chiwonongeko+ chimene Mulungu wakonzera anthu awa chidzabwera mwachilungamo ngati madzi osefukira,+