Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 26:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Kenako anthu onse+ a ku Yuda anatenga Uziya+ yemwe pa nthawiyo anali ndi zaka 16, n’kumulonga+ ufumu m’malo mwa bambo ake Amaziya.+

  • Yesaya 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Masomphenya+ amene Yesaya+ mwana wa Amozi anaona, okhudza Yuda ndi Yerusalemu m’masiku a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya,+ mafumu a Yuda:+

  • Hoseya 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Yehova analankhula+ ndi Hoseya+ mwana wa Beeri m’masiku+ a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya+ mafumu a Yuda, ndiponso m’masiku a Yerobowamu+ mwana wa Yowasi+ mfumu ya Isiraeli.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena