2 Mafumu 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Salumu mwana wa Yabesi anam’chitira chiwembu+ Zekariya n’kumupha+ ku Ibuleamu,+ ndipo iye anayamba kulamulira m’malo mwake. Hoseya 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Samariya adzaimbidwa mlandu+ chifukwa iye akupandukira Mulungu wake.+ Iwo adzagwetsedwa ndi lupanga.+ Ana awo adzaphwanyidwaphwanyidwa+ ndipo akazi awo amene ali ndi pakati adzatumbulidwa.”+
10 Ndiyeno Salumu mwana wa Yabesi anam’chitira chiwembu+ Zekariya n’kumupha+ ku Ibuleamu,+ ndipo iye anayamba kulamulira m’malo mwake.
16 “Samariya adzaimbidwa mlandu+ chifukwa iye akupandukira Mulungu wake.+ Iwo adzagwetsedwa ndi lupanga.+ Ana awo adzaphwanyidwaphwanyidwa+ ndipo akazi awo amene ali ndi pakati adzatumbulidwa.”+