-
Zekariya 14:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Anthu inu mudzathawira kuchigwa chimene chidzakhale pakati pa mapiri anga,+ chifukwa chakuti chigwacho chidzafika mpaka ku Azeli. Mudzathawa ngati mmene munachitira pothawa chivomezi chimene chinachitika m’masiku a Uziya, mfumu ya Yuda.+ Ndithu, Yehova Mulungu wanga adzabwera+ limodzi ndi oyera onse.+
-