Salimo 137:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Yehova, kumbukirani+ zimene ana a Edomu+ ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa,+Iwo anati: “Fafanizani mzindawo! Ufafanizeni mpaka pamaziko ake!”+ Ezekieli 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chifukwa chakuti Edomu walanga nyumba ya Yuda ndipo akupitiriza kuilanga ndi kuichitira zinthu zoipa kwambiri,+
7 Inu Yehova, kumbukirani+ zimene ana a Edomu+ ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa,+Iwo anati: “Fafanizani mzindawo! Ufafanizeni mpaka pamaziko ake!”+
12 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chifukwa chakuti Edomu walanga nyumba ya Yuda ndipo akupitiriza kuilanga ndi kuichitira zinthu zoipa kwambiri,+