-
Deuteronomo 24:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 “Pokolola mphesa m’munda wako, usabwerere kukakunkha zotsala. Mphesa zotsalazo zikhale za mlendo wokhala m’dziko lanu, mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye.
-