Genesis 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake. Deuteronomo 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Musawerengere anthu anu Aisiraeli mlanduwu, anthu amene munawawombola,+ inu Yehova, ndipo musaike mlandu wa magazi osalakwa+ pakati pa anthu anu Aisiraeli.’ Akatero mlandu wa magaziwo usakhale pa iwo.
6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake.
8 Musawerengere anthu anu Aisiraeli mlanduwu, anthu amene munawawombola,+ inu Yehova, ndipo musaike mlandu wa magazi osalakwa+ pakati pa anthu anu Aisiraeli.’ Akatero mlandu wa magaziwo usakhale pa iwo.