2 Mafumu 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zimenezi zinachitika chifukwa chakuti ana a Isiraeli anachimwira+ Yehova Mulungu wawo, yemwe anawatulutsa m’dziko la Iguputo+ n’kuwachotsa m’manja mwa Farao mfumu ya Iguputo, ndipo anayamba kuopa milungu ina.+ Yeremiya 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kodi sunadzichitire wekha zimenezi mwa kusiya Yehova Mulungu wako+ pa nthawi imene anali kukuyendetsa m’njira yake?+
7 Zimenezi zinachitika chifukwa chakuti ana a Isiraeli anachimwira+ Yehova Mulungu wawo, yemwe anawatulutsa m’dziko la Iguputo+ n’kuwachotsa m’manja mwa Farao mfumu ya Iguputo, ndipo anayamba kuopa milungu ina.+
17 Kodi sunadzichitire wekha zimenezi mwa kusiya Yehova Mulungu wako+ pa nthawi imene anali kukuyendetsa m’njira yake?+