Zekariya 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo iye anandiuza kuti: “Zinthu zimenezi zikuimira odzozedwa awiri+ amene amaimirira kumbali iyi ndi mbali inayi ya Ambuye wa dziko lonse lapansi.”+ Zekariya 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mngeloyo anandiyankha kuti: “Magaletawa akuimira zolengedwa zauzimu zinayi+ zakumwamba zimene zikubwera+ pambuyo poimirira pamaso pa Ambuye+ wa dziko lonse lapansi.+
14 Ndipo iye anandiuza kuti: “Zinthu zimenezi zikuimira odzozedwa awiri+ amene amaimirira kumbali iyi ndi mbali inayi ya Ambuye wa dziko lonse lapansi.”+
5 Mngeloyo anandiyankha kuti: “Magaletawa akuimira zolengedwa zauzimu zinayi+ zakumwamba zimene zikubwera+ pambuyo poimirira pamaso pa Ambuye+ wa dziko lonse lapansi.+