-
Yoswa 3:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Taonani! Likasa la pangano la Ambuye wa dziko lonse lapansi liyenda patsogolo panu kulowa mumtsinje wa Yorodano.
-
-
Mika 4:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 “Iwe mwana wamkazi wa Ziyoni,+ nyamuka upunthe tirigu pakuti nyanga* yako ndidzaisandutsa chitsulo. Ziboda zako ndidzazisandutsa mkuwa ndipo udzanyenyanyenya mitundu yambiri ya anthu.+ Phindu lawo limene apeza mwachinyengo udzalipereka kwa Yehova monga chinthu chopatulika.+ Zinthu zawo udzazipereka kwa Ambuye woona wa dziko lonse lapansi.”+
-