Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 6:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Siliva, golide, ndi zipangizo zamkuwa ndi zachitsulo, zonse n’zopatulika kwa Yehova.+ Ziyenera kupita ku chuma cha Yehova.”+

  • 2 Samueli 8:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Zinthu zimenezi Mfumu Davide inazipatulira Yehova pamodzi ndi siliva ndi golide wochokera ku mitundu yonse imene inagonjetsa.+

  • Yesaya 18:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Pa nthawi imeneyo, Yehova wa makamu+ adzapatsidwa mphatso ndi mtundu wa anthu ataliatali osalala, anthu oopedwa+ ndi mitundu yonse ya anthu. Umenewu ndi mtundu wa anthu amphamvu kwambiri, ndiponso wopambana pa nkhondo, umene nthaka yake yakokoloka ndi mitsinje. Mphatsoyo adzaiika kuphiri la Ziyoni, kumene kuli dzina la Yehova wa makamu.”+

  • Yesaya 23:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Phindu lake ndi malipiro ake+ zidzakhala zopatulika kwa Yehova. Phindu lakelo silidzasungidwa kapena kukundikidwa chifukwa malipiro ake adzakhala a anthu okhala pamaso pa Yehova,+ kuti anthuwo azidya mpaka kukhuta ndiponso kuti azivala zovala zokongola.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena