Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 8:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Taonani, ine ndi ana amene Yehova wandipatsa+ tili ngati zizindikiro+ ndiponso ngati zozizwitsa mu Isiraeli, zochokera kwa Yehova wa makamu amene amakhala m’phiri la Ziyoni.+

  • Yesaya 24:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mwezi wathunthu wachita manyazi. Dzuwa lowala lachitanso manyazi,+ pakuti Yehova wa makamu wakhala mfumu+ yaulemerero m’phiri la Ziyoni+ ndi mu Yerusalemu, pamaso pa anthu ake achikulire.+

  • Yoweli 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pamenepo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu,+ amene ndimakhala mu Ziyoni, phiri langa lopatulika.+ Yerusalemu adzakhala malo anga opatulika,+ ndipo alendo sadzadutsanso mmenemo.+

  • Mika 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Iwe mwana wamkazi wa Ziyoni,+ nyamuka upunthe tirigu pakuti nyanga* yako ndidzaisandutsa chitsulo. Ziboda zako ndidzazisandutsa mkuwa ndipo udzanyenyanyenya mitundu yambiri ya anthu.+ Phindu lawo limene apeza mwachinyengo udzalipereka kwa Yehova monga chinthu chopatulika.+ Zinthu zawo udzazipereka kwa Ambuye woona wa dziko lonse lapansi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena