Yesaya 41:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Taona! Ndakusandutsa chopunthira mbewu,+ chida chatsopano chopunthira mbewu chokhala ndi mano. Udzapondaponda mapiri n’kuwaphwanya, ndipo zitunda udzazisandutsa mankhusu.+ Yeremiya 51:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Mwana wamkazi wa Babulo ali ngati malo opunthira mbewu.+ Ino ndi nthawi yomupondaponda. Koma kwatsala ka nthawi pang’ono kuti nthawi yokolola imufikire.”+
15 “Taona! Ndakusandutsa chopunthira mbewu,+ chida chatsopano chopunthira mbewu chokhala ndi mano. Udzapondaponda mapiri n’kuwaphwanya, ndipo zitunda udzazisandutsa mankhusu.+
33 Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Mwana wamkazi wa Babulo ali ngati malo opunthira mbewu.+ Ino ndi nthawi yomupondaponda. Koma kwatsala ka nthawi pang’ono kuti nthawi yokolola imufikire.”+