Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 21:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Inu anthu anga amene mwapunthidwa ngati mbewu, ndi iwe mwana wa pamalo anga opunthira mbewu,+ zimene ndamva kwa Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, n’zimene ndakuuzani anthu inu.

  • Yesaya 41:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Taona! Ndakusandutsa chopunthira mbewu,+ chida chatsopano chopunthira mbewu chokhala ndi mano. Udzapondaponda mapiri n’kuwaphwanya, ndipo zitunda udzazisandutsa mankhusu.+

  • Amosi 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Yehova wanena kuti, ‘“Popeza kuti Damasiko+ anapanduka mobwerezabwereza,* sindidzamusinthira chigamulo changa. Sindidzamusinthira chigamulocho chifukwa chakuti anapuntha Giliyadi+ ndi zida zachitsulo zopunthira.

  • Mika 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Iwe mwana wamkazi wa Ziyoni,+ nyamuka upunthe tirigu pakuti nyanga* yako ndidzaisandutsa chitsulo. Ziboda zako ndidzazisandutsa mkuwa ndipo udzanyenyanyenya mitundu yambiri ya anthu.+ Phindu lawo limene apeza mwachinyengo udzalipereka kwa Yehova monga chinthu chopatulika.+ Zinthu zawo udzazipereka kwa Ambuye woona wa dziko lonse lapansi.”+

  • Habakuku 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Munadutsa m’dziko lapansi ndi kulidzudzula mwamphamvu. Inu mutakwiya munapuntha mitundu ya anthu ngati mbewu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena