Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 29:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako utenge mafuta odzozera+ ndi kuwathira pamutu pake ndi kum’dzoza.+

  • Hagai 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “‘Koma tsopano limba mtima iwe Zerubabele. Limba mtima+ iwe Yoswa mwana wa Yehozadaki mkulu wa ansembe,’ watero Yehova.

      “‘Limbani mtima anthu nonse a m’dzikoli ndipo gwirani ntchito,’+ watero Yehova.

      “‘Pakuti ine ndili ndi inu,’+ watero Yehova wa makamu.

  • 2 Akorinto 1:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Koma amene amatitsimikizira kuti inuyo ndi ife tili a Khristu, amenenso anatidzoza,+ ndiye Mulungu.

  • Chivumbulutso 11:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno ndidzachititsa mboni zanga ziwiri+ kunenera+ kwa masiku 1,260, zitavala ziguduli.”+

  • Chivumbulutso 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mboni zimenezi zikuimiridwa ndi mitengo iwiri ya maolivi,+ ndi zoikapo nyale ziwiri,+ ndipo mbonizo zaimirira pamaso pa Ambuye wa dziko lapansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena