Yesaya 59:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 N’chifukwa chake chilungamo chatitalikira kwambiri, ndipo zolungama sizikutipeza. Tinali kuyembekezera kuunika koma m’malomwake tikungoona mdima. Tinali kuyembekezera kuwala koma tikungoyendabe mu mdima wosatha.+ Yeremiya 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tinali kuyembekezera mtendere, koma panalibe chabwino chilichonse.+ Tinali kuyembekezera kuchiritsidwa, koma m’malomwake tinali kuona zinthu zochititsa mantha.+
9 N’chifukwa chake chilungamo chatitalikira kwambiri, ndipo zolungama sizikutipeza. Tinali kuyembekezera kuunika koma m’malomwake tikungoona mdima. Tinali kuyembekezera kuwala koma tikungoyendabe mu mdima wosatha.+
15 Tinali kuyembekezera mtendere, koma panalibe chabwino chilichonse.+ Tinali kuyembekezera kuchiritsidwa, koma m’malomwake tinali kuona zinthu zochititsa mantha.+