Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 4:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pamenepo ndinanena kuti: “Kalanga ine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Kunena zoona, mwapusitsa anthu awa+ ndiponso Yerusalemu mwa kunena kuti, ‘Mudzakhala pa mtendere,’+ koma lupanga lawabaya* mpaka mumtima.”

  • Yeremiya 14:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kodi Yuda mwamukaniratu,+ kapena kodi mukunyansidwa ndi Ziyoni?+ N’chifukwa chiyani mwatikantha popanda wotichiritsa?+ Anthu anali kuyembekezera mtendere, koma palibe chabwino chimene chachitika. Anali kuyembekezera nthawi yochiritsidwa, koma taonani, kukuchitika zoopsa zokhazokha.+

  • Mika 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mkazi wokhala ku Maroti anali kuyembekezera zinthu zabwino,+ koma zoipa zochokera kwa Yehova zafika pachipata cha Yerusalemu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena