Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 23:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pamenepo Balamu anayambanso kulankhula mwa ndakatulo, kuti:+

      “Nyamuka, Balaki iwe, tamvera.

      Tchera khutu kwa ine, iwe mwana wa Zipori.+

  • Yobu 27:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Tsopano Yobu anayambanso kulankhula mwandakatulo+ kuti:

  • Habakuku 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kodi anthu onsewa sadzamunenera mwambi,+ chining’a ndi mawu okuluwika? Wina adzanena kuti,

      “‘Kodi iye adzapitiriza kuchulukitsa zinthu zimene si zake+ kwa nthawi yaitali bwanji?+ Tsoka kwa iye pakuti akungochulukitsa ngongole yake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena