Yesaya 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 mudzanene mwambi uwu wotonza mfumu ya Babulo: “Uja ankagwiritsa ntchito anzakeyu wasiya ndithu! Wopondereza uja waleka ndithu!+ Mika 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa tsikulo munthu adzanena mwambi+ wokhudza anthu inu ndipo ndithu adzakuimbirani nyimbo ya maliro.+ Anthu adzanena kuti: “Ife talandidwa zinthu zathu!+ Cholowa cha anthu amtundu wathu chaperekedwa kwa anthu ena.+ Talandidwa cholowa chathu. Iye wapereka minda yathu kwa anthu osakhulupirika.”
4 mudzanene mwambi uwu wotonza mfumu ya Babulo: “Uja ankagwiritsa ntchito anzakeyu wasiya ndithu! Wopondereza uja waleka ndithu!+
4 Pa tsikulo munthu adzanena mwambi+ wokhudza anthu inu ndipo ndithu adzakuimbirani nyimbo ya maliro.+ Anthu adzanena kuti: “Ife talandidwa zinthu zathu!+ Cholowa cha anthu amtundu wathu chaperekedwa kwa anthu ena.+ Talandidwa cholowa chathu. Iye wapereka minda yathu kwa anthu osakhulupirika.”