Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti ndidzalirira mapiri mokweza ndi modandaula+ ndipo ndidzaimba nyimbo yoimba polira, pamene ndikulirira mabusa a m’chipululu. Ndidzalirira zimenezi chifukwa adzakhala atazitentha+ moti palibe munthu amene adzadutsamo. Anthu sadzamva kulira kwa ziweto+ m’mabusamo ndipo zolengedwa zouluka m’mlengalenga ngakhalenso nyama zidzakhala zitathawamo, zitachoka.+

  • Maliro 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Amene anali ndi anthu ambiri+ tsopano wakhala wopanda anthu.+

      Amene anali ndi anthu ambiri pakati pa mitundu ina+ wakhala ngati mkazi wamasiye.+

      Amene anali wolemekezeka pakati pa zigawo zina wayamba kugwira ntchito yaukapolo.+

  • Ezekieli 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Iye anautambasula pamaso panga, ndipo unalembedwa kuseri n’kuseri.+ Mumpukutumo munalembedwa nyimbo zoimba polira, mawu odandaula ndi mawu olira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena