Yeremiya 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti ku Ziyoni kwamveka anthu akulira mofuula kuti:+ “Tafunkhidwa!+ Tachita manyazi kwambiri! Pakuti tasiya dziko lathu ndiponso chifukwa atigwetsera nyumba zathu.”+ Yeremiya 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova wanena kuti: “Tsopano nditaya kutali anthu okhala padziko lapansi,+ ndipo ndiwachititsa kuvutika mtima kuti adziwe masautso awo.”+
19 Pakuti ku Ziyoni kwamveka anthu akulira mofuula kuti:+ “Tafunkhidwa!+ Tachita manyazi kwambiri! Pakuti tasiya dziko lathu ndiponso chifukwa atigwetsera nyumba zathu.”+
18 Yehova wanena kuti: “Tsopano nditaya kutali anthu okhala padziko lapansi,+ ndipo ndiwachititsa kuvutika mtima kuti adziwe masautso awo.”+