Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 18:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Mukapewa kuchita zimenezi, dziko silidzakusanzani chifukwa choliipitsa mmene lidzasanzira mitundu imene ikukhalamo musanafike inu.+

  • Levitiko 20:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “‘Motero inu muzisunga malangizo anga onse+ ndi zigamulo zanga zonse,+ kuti dziko limene ndikukulowetsani kuti mukhalemo lisakusanzeni.+

  • Maliro 4:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Anthu akuwafuulira kuti: “Chokani! Ndinu odetsedwa!+ Chokani! Chokani! Musatikhudze!”+

      Ansembe ndi aneneriwo alibe pokhala+ ndipo akungoyendayenda.+ Anthu a mitundu ina akunena kuti: “Amenewa sapitiriza kukhala kuno.+

  • Mika 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Nyamukani,+ chokani chifukwa ano si malo opumulirako.+ Dzikoli liwonongedwa chifukwa chakuti ladetsedwa+ ndipo kuwonongedwako kukhala kopweteka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena