Ekisodo 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Ndipo izi ndizo zigamulo zoti uwaikire:+ Deuteronomo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Mose anaitana Aisiraeli+ onse n’kuwauza kuti: “Inu Aisiraeli, mverani malangizo ndi zigamulo+ zimene ndikukuuzani lero, ndipo muziphunzire ndi kuzitsatira mosamala.+ Salimo 119:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Moyo wanga wasautsika chifukwa cholakalaka+Zigamulo zanu nthawi zonse.+ Yesaya 26:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Usiku, mtima wanga umakulakalakani.+ Ndithu ndimakufunafunani ndi mtima wonse,+ chifukwa mukadzaweruza dziko lapansi,+ anthu okhala panthaka ya dzikolo adzaphunzira chilungamo.+
5 Ndiyeno Mose anaitana Aisiraeli+ onse n’kuwauza kuti: “Inu Aisiraeli, mverani malangizo ndi zigamulo+ zimene ndikukuuzani lero, ndipo muziphunzire ndi kuzitsatira mosamala.+
9 Usiku, mtima wanga umakulakalakani.+ Ndithu ndimakufunafunani ndi mtima wonse,+ chifukwa mukadzaweruza dziko lapansi,+ anthu okhala panthaka ya dzikolo adzaphunzira chilungamo.+