Salimo 85:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzamvetsera zimene Mulungu woona Yehova adzanena,+Pakuti adzanena za mtendere kwa anthu ake+ ndi kwa okhulupirika ake.Koma iwo asadzidalire kwambiri ngati kale.+ 2 Akorinto 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndatero chifukwa mukufunafuna umboni wosonyeza kuti Khristu akulankhuladi mwa ine.+ Iye si wofooka kwa inu koma ndi wamphamvu pakati panu. Aheberi 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Kalekale, Mulungu analankhula ndi makolo athu nthawi zambiri+ ndiponso m’njira zambiri kudzera mwa aneneri.+
8 Ndidzamvetsera zimene Mulungu woona Yehova adzanena,+Pakuti adzanena za mtendere kwa anthu ake+ ndi kwa okhulupirika ake.Koma iwo asadzidalire kwambiri ngati kale.+
3 Ndatero chifukwa mukufunafuna umboni wosonyeza kuti Khristu akulankhuladi mwa ine.+ Iye si wofooka kwa inu koma ndi wamphamvu pakati panu.
1 Kalekale, Mulungu analankhula ndi makolo athu nthawi zambiri+ ndiponso m’njira zambiri kudzera mwa aneneri.+