Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Habakuku 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ine ndidzaimabe+ pamalo a mlonda ndiponso pakhoma lachitetezo. Ndidzakhala tcheru+ kuti ndione uthenga umene iye adzalankhula kudzera mwa ine+ ndi zimene ndidzayankha pamene iye akundidzudzula.+

  • Zekariya 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndidzawononga magaleta ankhondo mu Efuraimu ndiponso mahatchi mu Yerusalemu.+ Mauta omenyera nkhondo+ adzathyoledwa. Mfumuyo idzalankhula mawu amtendere kwa anthu a mitundu ina.+ Ulamuliro wake udzayambira kunyanja mpaka kukafika kunyanja. Ndiponso udzachokera ku Mtsinje* mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+

  • Aheberi 12:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Samalani kuti musasiye kumvetsera wolankhulayo.+ Pakuti ngati amene analephera kumvera wopereka chenjezo la Mulungu padziko lapansi sanapulumuke,+ kuli bwanji ifeyo? Nafenso sitidzapulumuka tikachoka kwa iye amene amalankhula ali kumwamba.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena