Salimo 49:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zokhumba za mtima wawo n’zakuti nyumba zawo zikhalebe mpaka kalekale,+Mahema awo akhalebe ku mibadwomibadwo.+Malo awo amawatcha mayina awo.+ Miyambo 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zinthu zamtengo wapatali za munthu wachuma ndizo mzinda wake wolimba,+ ndipo m’maganizo mwake zili ngati mpanda woteteza.+ Obadiya 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngakhale malo ako atakhala pamwamba ngati a chiwombankhanga, kapena ngakhale utamanga chisa chako pakati pa nyenyezi, ine ndidzakugwetsa kuchokera pamenepo,”+ watero Yehova.
11 Zokhumba za mtima wawo n’zakuti nyumba zawo zikhalebe mpaka kalekale,+Mahema awo akhalebe ku mibadwomibadwo.+Malo awo amawatcha mayina awo.+
11 Zinthu zamtengo wapatali za munthu wachuma ndizo mzinda wake wolimba,+ ndipo m’maganizo mwake zili ngati mpanda woteteza.+
4 Ngakhale malo ako atakhala pamwamba ngati a chiwombankhanga, kapena ngakhale utamanga chisa chako pakati pa nyenyezi, ine ndidzakugwetsa kuchokera pamenepo,”+ watero Yehova.