Deuteronomo 28:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova adzakulanga ndi chifuwa chachikulu,+ kuphwanya kwa thupi koopsa, kutupa, kutentha thupi kwambiri, lupanga,+ mphepo yotentha yowononga mbewu+ ndi matenda a mbewu.+ Zimenezi zidzakusautsa kufikira utawonongeka. Deuteronomo 32:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Adzalefuka ndi njala+ ndi kuwonongeka ndi matenda otentha thupi koopsa,+Ndi chiwonongeko chowawa.+Ndidzawatumizira zilombo za mano ataliatali,+Pamodzi ndi njoka zapoizoni za m’fumbi.+
22 Yehova adzakulanga ndi chifuwa chachikulu,+ kuphwanya kwa thupi koopsa, kutupa, kutentha thupi kwambiri, lupanga,+ mphepo yotentha yowononga mbewu+ ndi matenda a mbewu.+ Zimenezi zidzakusautsa kufikira utawonongeka.
24 Adzalefuka ndi njala+ ndi kuwonongeka ndi matenda otentha thupi koopsa,+Ndi chiwonongeko chowawa.+Ndidzawatumizira zilombo za mano ataliatali,+Pamodzi ndi njoka zapoizoni za m’fumbi.+