Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 21:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pamenepo Yehova anatumiza njoka zapoizoni pakati pawo,+ ndipo zinayamba kuwaluma moti Aisiraeli ambiri anafa.+

  • Yeremiya 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Inetu ndikutumiza njoka pakati panu, njoka zapoizoni,+ zimene simungaziimbire nyimbo kuti muziseweretse,+ ndipo zidzakulumani ndithu,” watero Yehova.

  • Amosi 9:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Akabisala pamwamba pa phiri la Karimeli, ndidzawafufuza mosamala ndi kuwatenga,+ ndipo akathawa pamaso panga ndi kubisala pansi pa nyanja,+ ndidzalamula njoka pansi pa nyanja pomwepo kuti iwalume.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena