Genesis 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’kupita kwa nthawi, mkaziyo anamuberekera Zimirani, Yokesani, Medani, Midiyani,+ Isibaki ndi Shuwa.+ Salimo 83:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muwachitire zimene munachitira Midiyani+ ndi Sisera.+Muwachitirenso zimene munachitira Yabini+ kuchigwa cha Kisoni.+
2 M’kupita kwa nthawi, mkaziyo anamuberekera Zimirani, Yokesani, Medani, Midiyani,+ Isibaki ndi Shuwa.+
9 Muwachitire zimene munachitira Midiyani+ ndi Sisera.+Muwachitirenso zimene munachitira Yabini+ kuchigwa cha Kisoni.+