Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 34:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Iwo sadzabedwanso ndi anthu a mitundu ina.+ Chilombo chakutchire sichidzawadyanso. Adzakhala mwabata popanda wowaopsa.+

  • Hoseya 2:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pa tsiku limenelo ndidzachita pangano ndi chilombo chakuthengo,+ cholengedwa chouluka m’mlengalenga ndi cholengedwa chokwawa panthaka, kuti ndithandize anthu anga. Ndidzathyola uta ndi lupanga ndipo ndidzathetsa nkhondo padziko.+ Pamenepo ndidzawachititsa kukhala mwabata.+

  • Mika 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Aliyense adzakhala pansi pa mtengo wake wa mpesa ndi mtengo wake wa mkuyu+ ndipo sipadzakhala wowaopsa,+ pakuti pakamwa pa Yehova wa makamu panena zimenezi.+

  • Chivumbulutso 7:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 chifukwa Mwanawankhosa,+ amene ali pambali pa mpando wachifumu, adzawaweta+ ndi kuwatsogolera ku akasupe a madzi+ a moyo. Ndipo Mulungu adzapukuta misozi yonse m’maso mwawo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena