1 Mafumu 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ayuda+ ndi Aisiraeli anapitiriza kukhala mwabata.+ Aliyense anali pansi pa mtengo wake wa mpesa ndi mtengo wake wa mkuyu,+ kuchokera ku Dani mpaka ku Beere-seba,+ masiku onse a Solomo. Zekariya 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Pa tsiku limenelo mudzaitanizana, aliyense atakhala pansi pa mtengo wake wa mpesa ndiponso wa mkuyu,’+ watero Yehova wa makamu.”
25 Ayuda+ ndi Aisiraeli anapitiriza kukhala mwabata.+ Aliyense anali pansi pa mtengo wake wa mpesa ndi mtengo wake wa mkuyu,+ kuchokera ku Dani mpaka ku Beere-seba,+ masiku onse a Solomo.
10 “‘Pa tsiku limenelo mudzaitanizana, aliyense atakhala pansi pa mtengo wake wa mpesa ndiponso wa mkuyu,’+ watero Yehova wa makamu.”