Mateyu 25:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mitundu yonse ya anthu idzasonkhanitsidwa kwa iye+ ndipo adzalekanitsa+ anthu,+ mmene m’busa amalekanitsira nkhosa ndi mbuzi. Yohane 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndine m’busa wabwino.+ M’busa wabwino amataya moyo wake chifukwa cha nkhosa.+
32 Mitundu yonse ya anthu idzasonkhanitsidwa kwa iye+ ndipo adzalekanitsa+ anthu,+ mmene m’busa amalekanitsira nkhosa ndi mbuzi.