Yoweli 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Konzekerani nthawi yosala kudya.+ Itanitsani msonkhano wapadera.+ Sonkhanitsani pamodzi akulu ndi anthu onse okhala m’dzikoli kuti akumane kunyumba ya Yehova Mulungu wanu+ ndipo alirire Yehova kuti awathandize.+ Yoweli 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sonkhanitsani anthu onse pamodzi ndipo muyeretse mpingo.+ Sonkhanitsani amuna achikulire. Sonkhanitsani pamodzi ana ndi makanda oyamwa.+ Mkwati atuluke m’chipinda chake ndipo mkwatibwi atuluke kumalo ake ogona.
14 Konzekerani nthawi yosala kudya.+ Itanitsani msonkhano wapadera.+ Sonkhanitsani pamodzi akulu ndi anthu onse okhala m’dzikoli kuti akumane kunyumba ya Yehova Mulungu wanu+ ndipo alirire Yehova kuti awathandize.+
16 Sonkhanitsani anthu onse pamodzi ndipo muyeretse mpingo.+ Sonkhanitsani amuna achikulire. Sonkhanitsani pamodzi ana ndi makanda oyamwa.+ Mkwati atuluke m’chipinda chake ndipo mkwatibwi atuluke kumalo ake ogona.