20 khamu lonse la anthu a mitundu yosiyanasiyana, mafumu onse a dziko la Uzi,+ mafumu onse a dziko la Afilisiti,+ Asikeloni,+ Gaza,+ Ekironi+ ndi otsala onse a ku Asidodi,+
5 Gaza+ adzameta mpala+ chifukwa cha chisoni. Asikeloni+ amuwononga ndi kumukhalitsa chete. Inu otsala a m’chigwa cha Gaza ndi Asikeloni, mudzadzichekacheka kufikira liti?+